| ◆ الترحيب وتعريف الإسلام |
|---|
| Takulandilani patsamba lathu, Ndine wokondwa kugawana nanu tanthauzo la Chisilamu. |
Chisilamu chikutanthauza ➡️ kugonjera kwathunthu ndi kumvera Mulungu.
Aliyense amene apereka chifuniro chake kwa Mulungu ndi Msilamu.
Chisilamu chinabweretsa mtendere ndi chisangalalo m'mitima ya anthu mamiliyoni ambiri, ndipo inunso mukhoza kukhala m'modzi wa iwo. | | ◆ التوحيد | | Ife timakhulupirira kuti Mulungu ndi mmodzi ndipo alibe wothandizana naye.
Iye ali ndi mphamvu Yangwiro, kumva ndi kuona.
Mulungu yekha ndi amene amakhululukira machimo.
🌴" Allah” ndi Mulungu Wamphamvuyonse, Mlengi. | | ◆ الإيمان بالرسل وسيدنا محمد صلى الله عليه وسلم والقرآن | | Mulungu adatumiza atumiki kuti adzaitane anthu kuti apembedze Mulungu yekha, monga Adam, Ibrahim, Mose, Yesu ndi Muhammad.
Muhammad (SAW) ndi womaliza mwa Atumiki ochokera kwa Mulungu kupita kwa anthu.
Muhammad (SAW) adadza ndi chivumbulutso chomaliza chomwe ndi Quran. | | ◆ عقيدتنا في عيسى عليه السلام (ترسل مقسمة) | | 1. Asilamu onse amakhulupilira ndi kumukonda Yesu (Mtendere ukhale pa Iye).
2. Yesu ndi mthenga waumunthu wochokera kwa Mulungu, monganso Adamu.
Iye si Mulungu ndipo si mwana wa Mulungu.
Mulungu anapatsa Yesu zozizwitsa. | | 5. Mulungu Wamphamvuyonse adapulumutsa Mose kwa Farao. Anapulumutsa Abrahamu kumoto. Ndipo anapulumutsa Yesu kwa Ayuda amene ankafuna kumupachika ndi kumupha.
Mulungu anaukitsa Yesu kumwamba, ndipo Yesu adzabweranso kudzapha okana Khristu.
Yesu ndi Muhammad (SAW) ndi Atumiki ndi akapolo a Mulungu, adatumidwa kuti atsogolere anthu kuti apembedze Allah. | | ◆ تأكيد على أهم النقاط وبقية أركان الإيمان | | Kumbukirani:
Timapembedza ndi kupemphera kwa Allah. 2.Sitipemphera kwa Yesu kapena kwa Muhammad
Tikupempha chikhululuko kwa Mulungu Yemwe adatilenga.
Ife timakhulupirira angelo ndi tsiku lachiweruzo. | | ◆الأسئلة قبل عرض الشهادة | | (1) Yesu ndindani?
Mulungu
Mwana wa Mulungu .
Wolemekezeka, Mneneri wamunthu
(2) Timapembedza:
(3) Muhammed ndani?