#الإيمان_بالملائكة
Asilamu amakhulupirira kuti angelo alipo komanso kuti ndi zolengedwa zolemekezeka.
Angelo amalambira Mulungu yekha, amamvera Iye, ndipo amachita zinthu motsatira lamulo Lake basi.
Mwa angelo pali Gabriyeli, amene adatsitsa Qur’an kwa Muhammad .