Kodi mungayankhe mafunso awa musanakuonjezereni ku gulu lophunzirira 👇🏾

| 1️⃣ Yesu ndi ndani ? (a) Mulungu (b) Mwana wa Mulungu

(c) Mneneri
2️⃣ Muhammad ndi ndani ?
(a) Mneneri womaliza wa Mulungu.
(b) Sindikudziwa.
3️⃣ Kodi buku lomaliza la Mulungu ndi liti ?
(a) Qur'an yopatulika
(b) Baibulo
(c) Sindikudziwa